الرئيسيةLatestUlosi wa Prophet Rodrick Mtupa wakwanilitsidwa LatestNation Ulosi wa Prophet Rodrick Mtupa wakwanilitsidwa 0 241 22 November 2023 كتب بواسطة Malawi Observer شارك FacebookTwitterPinterestWhatsApp Kanema yemwe wafala kwambiri pa masamba a mchezo a Facebook ndi Whatsapp akuonetsa, munthu wa Mulungu Prophet Rodrick Mtupa, akulotsera zomwe zachitika dzulo ku Limbe mu Mzinda wa Blantyre komwe apolisi komanso ogwira ntchito ku khonsolo ya mzinda wu anayendesedwa wa uyo! Uyo! ndi anthu okwiya.Apolisi-wa anawona za malozazi pa nthawi yomwe anapita ku msika wa Limbe ndi cholinga chokagwira a malonda (Ma Vendor) omwe amachita malonda awo m’malo osayenera; komatu phuno salota, osaka-wa anasanduka wosakidwa pomwe ochita malonda okwiya wa anayamba kuwagenda mpaka kuthawa liwilo la mtondo wodowoka.Koma malingana ndi Kanema amene anthu akugawana pa makina a internet, zomwe zachitika ku Limbe zinalotseredwa kale ndi Prophet Mtupa a utumiki wa Holy Palace Cathedral International, kutero kuti panalibe cha chilendo.“Kuzakhala kuukira kwa anthu; ndipo m’maso anga auzimu ndikuwona gulu la anthu litagwirana manja ndi kumagenda anthu a boma(a polisi komanso ogwira ntchito ku city), izi zichitika ndithu,” anatero Prophet Mtupa mu Ulosi wawo wa kumayambiliro a chaka chino, akulotsera zomwe zachitika dzulo lachiwiri ku Limbe.Pakadali pano, Mneneri wa apolisi ya Limbe Aubrey Singayamwa wati apolisi akhazikitsa kafukufuku wawo kufuna kumanga anthu omwe anayambitsa ziwawazi, ndipo pofika lero lachitatu apolisi-wa amanga anthu okwana anayi. شارك FacebookTwitterPinterestWhatsApp المادة السابقةBSC Team One retain Ethco Ladies championshipالمقالة القادمةNBS Bank shines, scoops 3 Global Brand Magazine awards Malawi Observerhttp://malawiobservers.com مقالات ذات صلة Latest Sponsors, FAM delights in Castel Cup outcome 23 December 2024 Latest Castel Malawi sets mood for Castel Cup final 20 December 2024 Latest Fired PCL executives file K33bn claim for unfair dismissal and unlawful labour practices 20 December 2024 ترك الرد إلغاء الرد التعليق: من فضلك ادخل تعليقك اسم:* من فضلك ادخل اسمك هنا البريد الإلكتروني:* لقد أدخلت عنوان بريد إلكتروني غير صحيح! الرجاء إدخال عنوان بريدك الإلكتروني هنا الموقع: احفظ اسمي والبريد الإلكتروني وموقع الويب في هذا المتصفح للمرة الأولى التي أعلق فيها. Δ - Advertisment - الأكثر شهرة Sponsors, FAM delights in Castel Cup outcome 23 December 2024 Castel Malawi sets mood for Castel Cup final 20 December 2024 Fired PCL executives file K33bn claim for unfair dismissal and unlawful labour practices 20 December 2024 Journalists gain insights on Responsible Gambling through MAGLA Training 19 December 2024 تحميل أكثر احدث التعليقات Jaffali Wilson على POLL: Was it right for Fleetwood Haiya to coordinate football hooliganism against FAM President Walter Nyamilandu? youtube على EXPOSED: Cleophas, Masophenya shielding Grimatta in the Emmilie mysterious death…Bribes Police IG, MCP officials Samuel Sibuni على State House Begs For Mercy As ACB Summons PM Mkaka, SPC Chikhosi Samuel Sibuni على State House Begs For Mercy As ACB Summons PM Mkaka, SPC Chikhosi Dzonzi Yoffat على State House Begs For Mercy As ACB Summons PM Mkaka, SPC Chikhosi Fumbi ndiwe mwini على Disgruntled Intelligence Officers Threaten To Boycott Work Over Nepotism Ndaziona على Malawi’s Guptas’ Master Abdullah, Deepak implicated in Baroda Loan Bill Smuggling Scandal John Kapito على Malawi’s Guptas’ Master Abdullah, Deepak implicated in Baroda Loan Bill Smuggling Scandal Warm Heart على Malawi’s Guptas’ Master Abdullah, Deepak implicated in Baroda Loan Bill Smuggling Scandal Paramount على Malawi’s Guptas’ Master Abdullah, Deepak implicated in Baroda Loan Bill Smuggling Scandal Fakili Omar على Malawi’s Guptas’ Master Abdullah, Deepak implicated in Baroda Loan Bill Smuggling Scandal Chrissy Njinkho على Malawi’s Guptas’ Master Abdullah, Deepak implicated in Baroda Loan Bill Smuggling Scandal Ibrahim على BREAKING NEWS: MCP’s Mkaka wants to open own bank Nakonyani على Chakwera’s Justice Minister Mvalo humiliates Malawi in Geneva: Speaks to 1490 empty seats